Back to Top

Don Intellect Shakur - Sukulu Yolepheleka Lyrics

Don Intellect Shakur - Sukulu Yolepheleka Lyrics
Official

Ooh my God Nefter
Stephen, this is Dawson Elementary Middle School
The mother of a 13-year-old 8th grader says yes, her son is in trouble because he tried to step in and help another student
Knawledge what up baby
Mzanga yekhayo waku Chilinde
Anamubweza kugeli, fukwa fees sanalipire
Kwawo kunali kwa dolla, mdala yake isanatisiye
Ankala yekha achibale kunalibe
Ankaona mowa, chamba nzomwe zingamuthandize
Zachisoni pano analowa tchire
Mzanga wina anali waku Kawale
Sanali Yo, tinkamutcha mzimwale
Nthawi yadzinja ankatenga misale
Koma ana marra, sanamalize maphuzilo a sekondale
Waku Kaliyeka cha pa manda
Mclass anali shasha
Panalibe babe yoti sinkamuwaza
Onse anali nkhwanga, tinkamutcha shatta
Maths, Bio, zambiri sankatsata
Jokes yokhayo, class inkango khafa
Komwe anapita, palibe akudziwa
Tinangomva mbiri anapeleka mimba
Njira, ndizambiri m'mene sukulu imathela
Tsogolo lowala limalepheleka
Umphawi, imfa, ndi chibwana
Zibwezi uli mwana
Izi ndi zina, zomwe zimachitika
Sisewelo, zimachitika
Ndizambiri zimachita
Sukulu umasiya
Ndizambiri zingachitike
Sukulu ndikusiya
Mzanga Limba
Dolo kwambiri, wakutha kuyimba
Break yachiwiri, ayi sankafika
Aphuzitsi ankamulangiza
Koma sankasintha
Mfana ovuta, chomwe ankafuna ndikutchuka
Notes analibe mclass ankamutulutsa
Lomwe anali nalo ndi kope lama rhames
Tsiku lina sanabwele, two terms sanagele
Afuna amveke on made on Monday koma Joy sana player
Mpaka lero akupusha career
Nde kunali Maria, mkazi owala, ovuta kugwira
Mkazi odzimva, koma odziwa kutchila
Number 1, pa top samatsika
Chosadziwa amayenda ndi sala
Anamupatsa phaa, pano amamwaso mankhwala
N'zake wa Jane, paja ndaa
Mmmh ndangoiwala dzina lake lenileni
Komwe ankakhala sanali abale ake eni eni
Ankamuzuza, ankamuuza
Mayeso sangakhoze, angozivutitsa
Nde sukulu anango dropa ndiku suntha
Nkupeza mamuna
Adakatani, adasiya geli adakayifuna
Njira, ndizambiri m'mene sukulu imathela
Tsogolo lowala limalepheleka
Umphawi, imfa, ndi chibwana
Zibwezi uli mwana
Izi ndi zina, zomwe zimachitika
Sisewelo, zimachitika
Ndizambiri
Ndizambiri zimachita
Sukulu umasiya
Ndizambiri zingachitike
Sukulu ndikusiya
My son grabbed the teacher's shirt to try to pull him off of the child
He said, when I asked him, I said, you know, why did you do that
He was like, Mom, he could not breathe
He was gasping for air
And he was like, I had to do something
I said, were there other administrators around
He said yes, but no one was intervening
The alleged incident happened in a hallway outside a classroom late in the school day
We reached out to the school's principal, who has not returned our call
[ Correct these Lyrics ]

We currently do not have these lyrics. If you would like to submit them, please use the form below.

Writer: Blessings Mtsiriza
Copyright: Lyrics © O/B/O DistroKid

Don Intellect Shakur - Sukulu Yolepheleka Video
(Show video at the top of the page)

Performed By: Don Intellect Shakur
Language: English
Length: 3:54
Written by: Blessings Mtsiriza

Tags:
No tags yet