Wazizur
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Uluruwu ndiye sukuchoka
Cancer yi ngati ndingofa mwina ndizachila koma
Si lero
Ndaona zinthu ngati Doctor
Mmanjamu anthu kumangofa Ndufuna ntapuma koma
Si lero
I know lero sizingatheke
Pa wheelchair'Pa one day ndizachokapo
Inde ngakhale
Si lero
Masten anga kuli Chete
Munapita ngati Bodza Nzakuonaninso ngakhale
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Mufunse Driemo
Made it outta Ntchisi ena nkumati si iyeyo
Nawenso uzaiphula Aise ngakhale si lero
Nzothekanso kufa usanaiphulire ndiye Moyo
Ma funso onse azayankhidwa ngakhale si lero
Wina akuyendera Manja fukwa alibe Miyendo
Amasamala ziweto
Suli wekha tiyeko
Ikanso ma earphone ndimvetsele mavutowa azatha ngakhale
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero
Si lero and I still believe
Though not today
Though not today
Though not today
Si lero
Si lero
Si lero